Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 20:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono mithenga ija inabwerera, niti, Atero Benihadadi, kuti, Ndinatumadi kwa iwe, ndi kuti, Uzindipatsa siliva wako, ndi golidi wako, ndi akazi ako, ndi ana ako;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 20

Onani 1 Mafumu 20:5 nkhani