Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 20:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo awa anakhala m'misasa pandunji pa ajawo masiku asanu ndi awiri. Tsono kunali, tsiku lacisanu ndi ciwiri anayambana nkhondo; ndipo ana a Israyeli anaphako Aaramu tsiku limodzi anthu oyenda pansi zikwi zana limodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 20

Onani 1 Mafumu 20:29 nkhani