Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 20:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthu uja wa Mulungu anafikako, nalankhula ndi mfumu ya Israyeli, nati, Atero: Yehova, Popeza Aaramu amati, Yehova ndiye Mulungu wa kumapiri, osati Mulungu wa kuzigwa, mwa ici ndidzapereka unyinji uwu waukuru m'dzanja mwako, kuti mudziwe kuti Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 20

Onani 1 Mafumu 20:28 nkhani