Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 20:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Benihadadi anatuma kwa iye, nati, Milungu indilange, nionjezepo, ngati pfumbi la Samaria lidzafikira kudzaza manja a anthu onse akutsata mapazi anga.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 20

Onani 1 Mafumu 20:10 nkhani