Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 2:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo taona uli naye Simeyi mwana wa Gera wa pfuko la Benjamini wa ku Bahurimu, yemwe uja adanditemberera ndi temberero lalikuru tsiku lija lakupita ine ku Mahanaimu; koma anadzakomana ndi ine pa Yordano, ndipo ndinalumbirira iye pa Yehova, kuti, Sindikupha iwe ndi lupanga,

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2

Onani 1 Mafumu 2:8 nkhani