Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 19:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iye, Ndacitira cangu Yehova Mulungu wa makamu; popeza ana a Israyeli ataya cipangano canu, nagumula maguwa a nsembe anu, napha aneneri anu ndi lupanga; ndipo ndatsala ndekha, ndipo afuna moyo wanga kuucotsa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 19

Onani 1 Mafumu 19:14 nkhani