Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 18:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndi miyalayi anamanga guwa la nsembe m'dzina la Yehova, nazunguniza guwalo ndi mcera, ukulu wace ngati kulandira miyeso iwiri ya mbeu kuzinga guwalo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:32 nkhani