Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 18:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Eliya ananena ndi aneneri a Paala, Dzisankhireni ng'ombe imodzi yanu, muyambe kuikonza, popeza mucuruka; nimuitane dzina la mulungu wanu, koma musasonkhepo moto.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:25 nkhani