Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 16:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'masiku ace Hiyeli wa ku Beteli anamanga Yeriko; pokhazika maziko ace anadzifetsera Abiramu mwana wace woyamba, poimika zitseko zace anadzifetsera Zegubi mwana wace wotsiriza; monga mwa mau a Yehova amene ananenetsa Yoswa mwana wa Nuni.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 16

Onani 1 Mafumu 16:34 nkhani