Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 16:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ahabu anapanganso cifanizo; ndipo Ahabu amene anapambana mafumu onse a Israyeli adamtsogolerawo, kuputa mkwiyo wa Yehova Mulungu wa Israyeli,

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 16

Onani 1 Mafumu 16:33 nkhani