Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 16:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anagula kwa Semeri citunda ca Samaria ndi matalente awiri a siliva, namanga pacitundapo, nacha dzina lace la mudzi anaumanga Samaria, monga mwa dzina la Semeri mwini citundaco.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 16

Onani 1 Mafumu 16:24 nkhani