Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 14:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo macitidwe ena a Yerobiamu m'mene umo anacitira nkhondo, ndi m'mene umo anacitira ufumu, taona, analembedwa m'buku la macitidwe a mafumu a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 14

Onani 1 Mafumu 14:19 nkhani