Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 13:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anapatsa cizindikilo tsiku lomwelo, nari, Cizindikilo cimene Yehova ananena ndi ici, Taonani guwali la nsembe lidzang'ambika, ndi phulusa liri pa ilo lidzatayika.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13

Onani 1 Mafumu 13:3 nkhani