Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 12:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yerobiamu anaika madyerero mwezi wacisanu ndi citatu, tsiku lakhumi ndi cisanu la mwezi olingana ndi madyerero aja a ku Yuda, napereka nsembe pa guwa la nsembe; anatero m'Beteli, nawaphera nsembe ana a ng'ombe aja anawapanga, naika m'Beteli ansembe a misanje imene anaimanga.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 12

Onani 1 Mafumu 12:32 nkhani