Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 12:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova atero, Musamuka, ndipo musakayambana ndi abale anu ana a Israyeli, bwererani yense kunyumba kwace; popeza cinthuci cacokera kwa Ine. Ndipo iwo anamvera mau a Yehova, natembenuka, nabwerera monga mwa mau a Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 12

Onani 1 Mafumu 12:24 nkhani