Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 12:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, popeza atate wanga anakusenzani gori lolemera, ine ndidzaonjezerapo pa gori lanu, atate wanga anakukwapulani ndi zikoti, koma ine ndidzakukwapulani ndi zinkhanira.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 12

Onani 1 Mafumu 12:11 nkhani