Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 11:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali nthawi yomweyo kuti Yerobiamu anaturuka m'Yerusalemu, ndipo mneneri Ahiya wa ku Silo anampeza m'njira; tsono iyeyo anabvaliratu cobvala catsopano, ndipo iwo awiri anali okha kuthengo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 11

Onani 1 Mafumu 11:29 nkhani