Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 11:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Hadadi uja anathawa, iyeyo ndi a ku Edomu ena, akapolo a atate wace pamodzi naye, kumka ku Aigupto, Hadadiyo akali mwana.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 11

Onani 1 Mafumu 11:17 nkhani