Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 11:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anamuutsira Solomo mdani, ndiye Hadadi M-edomu; iyeyo anali wa mbumba ya mfumu ya ku Edomu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 11

Onani 1 Mafumu 11:14 nkhani