Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 10:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akavalo a Solomo anacokera ku Aigupto; anthu a malonda a mfumu anawagula magulu magulu, gulu liri lonse mtengo wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 10

Onani 1 Mafumu 10:28 nkhani