Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 10:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akafika munthu yense ndi mtulo wace, zotengera zasiliva, ndi zotengera zagolidi, ndi zobvala, ndi zida, ndi zonunkhira, ndi akavalo, ndi nyuru; momwemo caka ndi caka.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 10

Onani 1 Mafumu 10:25 nkhani