Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 10:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nafika ku Yerusalemu ndi ulendo wace waukulu, ndi ngamila zakunyamula zonunkhira, ndi golidi wambiri, ndi timiyala ta mtengo wapatali; ndipo atafika kwa Solomo anakamba naye zonse za m'mtima mwace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 10

Onani 1 Mafumu 10:2 nkhani