Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 1:47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso akapolo a mfumu anadzadalitsa Davide mbuye wathu mfumu, nati, Mulungu wanu aposetse dzina la Solomo lipunde dzina lanu, nakulitse mpando wace wacifumu upose mpando wanu wacifumu; ndipo mfumu anawerama pakamapo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:47 nkhani