Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 1:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza iye watsika lero, nakapha ng'ombe ndi nyama zonona ndi nkhosa zaunyinji, naitana ana amuna onse a mfumu, ndi akazembe a nkhondo, ndi Abyatara wansembe; ndipo taonani, iwowo akudya ndi kumwa pamaso pace, nati, Akhale ndi moyo mfumu Adoniya.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:25 nkhani