Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 1:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Natani anati, Mbuye wanga mfumu, kodi inu munati, Adoniya adzakhala mfumu nditamuka ine, nadzakhala ndiye pa mpando wanga wacifumu?

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:24 nkhani