Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 1:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anapha ng'ombe ndi nyama zonona ndi nkhosa zaunyinji, naitana ana amuna onse a mfumu, ndi Abyatara wansembe, ndi Yoabu kazembe wa nkhondo; koma Solomo mnyamata wanu sanamuitana.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:19 nkhani