Ameneyo anatsata Paulo ndi ite, napfuula, kuti, Anthu awa ndi akapolo a Mulungu wa Kumwambamwamba amene akulalikirani inu njira ya cipulumutso.