Zekariya 5:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Pamenepo ndinakwezanso maso anga, ndinapenya, taonani, mpukutu wouluka. Ndipo anati kwa ine, Uona ciani? Ndipo