Ndipo kudzakhala, akaima mapazi a ansembe akusenza likasa la Yehova Ambuye wa dziko lonse, m'madzi a Yordano, adzadulidwa madziwo, ndiwo madzi ocokera kumagwero, nadzaima mulu umodzi.