Ndipo Yoswa anati kwa ana a Israyeli, Mucedwa mpaka liti kulowa ndi kulandira dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu anakupatsani?