Yobu 26:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Koma Yobu anayankha, nati, Wafotokozera yani mau?Ndi mzimu wa yani unaturuka mwa iwe?