Mau amene ananena Yeremiya mneneri kwa Baruki mwana wace wa Neriya, pamene analemba mau awa m'buku ponena Yeremiya, caka cacinai ca Yehoyakimu mwana wace wa Yosiya, mfumu ya Yuda, ndi kuti,