Tinawagwetsa; Hesiboni waonongeka kufikira ku Diboni,Ndipo tinawapululutsa kufikira ku Nofa,Ndiwo wakufikira ku Medeba.