Yehova acita ufumu; wadzibveka ndi ukulu;Wadzibveka Yehova, wadzimangirira mphamvu m'cuuno;Dziko lomwe lokhalamo anthu likhazikika, silidzagwedezeka.