Ndidzayimbira zacifundo za Yehova nthawi yonse:Pakamwa panga ndidzadziwitsira cikhulupiriko canu ku mibadwo mibadwo.