Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 89:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndidzayimbira zacifundo za Yehova nthawi yonse:Pakamwa panga ndidzadziwitsira cikhulupiriko canu ku mibadwo mibadwo.

2. Pakuti ndinati, Cifundo adzacimanga kosaleka;Mudzakhazika cikhulupiriko canu m'Mwamba mweni mweni.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 89