M'kamwa mwa makanda ndi oyamwamunakhazikitsamphamvu,Cifukwa ca otsutsana ndi Inu,Kuti muwaletse mdani ndi wobwezera cilango.