Koma mfumu idzakondwera mwa Mulungu;Yense wakulumbirira iye adzatamandira;Pakuti pakamwa pa iwo onena bodza padzatsekedwa.