Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 63:10-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

10. Adzawapereka ku mphamvu ya lupanga;Iwo adzakhala gawo la ankhandwe.

11. Koma mfumu idzakondwera mwa Mulungu;Yense wakulumbirira iye adzatamandira;Pakuti pakamwa pa iwo onena bodza padzatsekedwa.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 63