Pamenepo anaopa kwakukuru, popanda cifukwa ca kuopa:Pakuti Mulungu anamwaza mafupa a iwo akuzinga iwe;Unawacititsa manyazi, pakuti Mulungu anawakaniza.