Amuna inu, ulemu wanga udzakhala wamanyazi kufikira liti?Mudzakonda zacabe, ndi kufunafuna bodza kufikira liti?