Pakuti mkwiyo wace ukhala kanthawi kokha;Koma kuyanja kwace moyo wonse:Kulira kucezera,Koma mamawa kuli kupfuula kukondwera.