Musandipereke ku cifuniro ca akundisautsa;Cifukwa zinandiukira mboni zonama ndi iwo akupumira zaciwawa.