Yehova ndiye kuunika kwanga ndi cipulumutso canga; ndidzaopa yani?Yehova ndiye mphamvu ya moyo wanga; ndidzacita mantha ndi yani?