Pakuti mdani alondola moyo wanga;Apondereza pansr moyo wanga;Andikhalitsa mumdima monga iwo adafa kale lomwe.