Anthu anu adzadzipereka eni ace tsiku la camuna canu:M'moyera mokometsetsa, mobadwira tnatanda kuca,Muli nae mame a ubwana wanu.