Pakuti pakamwa pa woipa ndi pakamwa pa cinyengo pananditsegukira;Anandilankhulira ndi m'kamwa mwa bodza.