Zoipa zao zonse zidze pamaso panu,Muwacitire monga mwandicitira ine cifukwa ca zolakwa zanga zonse,Pakuti ndiusa moyo kwambiri, ndi kulefuka mtima wanga,