Iwo anamva kuti ndiusa moyo, palibe wonditonthoza;Adani anga onse atha kumva msauko wanga, nakondwera kuti mwatero ndinu;Mudzafikitsa tsiku lija mwalichula, ndipo iwowo adzanga ine.