Ziyoni atambasula manja ace, palibe wakumtonthoza;Yehova walamulira kuti omzungulira Yakobo akhale adani ace;Yerusalemu wasanduka cinthu conyansa pakati pao.